31 Ndipo khamulo linawaletsa, kuti atonthole: koma anakuwitsa, nanena, Ambuye, muticitire cifundo, Inu Mwana wa Davide.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 20
Onani Mateyu 20:31 nkhani