Mateyu 20:8 BL92

8 Ndipo pamadzulo, mwini munda anati kwa kapitao wace, Kaitane anchito, nuwapatse iwo kulipira kwao, uyambe kwa omarizira kufikira kwa oyamba.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 20

Onani Mateyu 20:8 nkhani