15 Koma ansembe akuru ndi alembi, m'mene anaona zozizwitsa zomwe Iye anazicita, ndi ana alinkupfuula kuKacisiko kuti, Hosana kwa Mwana wa Davide, anapsa mtima,
Werengani mutu wathunthu Mateyu 21
Onani Mateyu 21:15 nkhani