28 Nanga mutani? Munthu anali cao ana awiri; nadza iye kwa woyamba nati, Mwanawe, kagwire lero nchito ku munda wampesa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 21
Onani Mateyu 21:28 nkhani