27 Ndipo anamyankha Yesu, nati, Sitidziwa ife. Iyenso ananena nao, lnenso sindikuuzani ndi ulamuliro wotani ndizicita izi.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 21
Onani Mateyu 21:27 nkhani