36 Anatumizanso akapolo ena, akucuruka oposa akuyambawa; ndipo anawacitira iwo momwemo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 21
Onani Mateyu 21:36 nkhani