Mateyu 21:35 BL92

35 Ndipo olimawo anatenga akapolo ace, nampanda mmodzi, wina namupha, wina namponya miyala.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 21

Onani Mateyu 21:35 nkhani