Mateyu 21:34 BL92

34 Ndipo pamene nyengo ya zipatso inayandikira, anatumiza akapolo ace kwa olima mundawo, kukalandira zipatso zace.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 21

Onani Mateyu 21:34 nkhani