Mateyu 22:13 BL92

13 Pomwepo mfumu inati kwa atumiki, Mumange iye manja ndi miyendo, mumponye ku mdima wakunja; komweko kudzali kulira ndi kukukuta mano.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 22

Onani Mateyu 22:13 nkhani