44 Ambuye ananena kwa Ambuye wanga,Ukhale pa dzanja lamanja langa,Kufikira Ine ndidzaika adani ako pansi pa mapazi ako.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 22
Onani Mateyu 22:44 nkhani