45 Cifukwa cace ngati Davide amchula Iye Ambuye, ali mwana wace bwanji? Ndipo panalibe mmodzi anatha kumyankha mau.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 22
Onani Mateyu 22:45 nkhani