16 Tsoka inu, atsogoleri akhungu, amene munena, Amene ali yense akalumbira kuchula Kacisi, palibe kanthu; koma amene akalumbira kuchula golidi wa Kacisi, wadzimangirira.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 23
Onani Mateyu 23:16 nkhani