17 Inu opusa, ndi akhungu: pakuti coposa nciti, golidi kodi, kapena Kacisi amene ayeretsa golidiyo?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 23
Onani Mateyu 23:17 nkhani