25 Tsoka inu, alembi ndi Afarisi, onyenga! cifukwa mutsuka kunja kwace kwa cikho ndi mbale, koma m'katimo iwo adzala ndi kulanda ndi kusadziletsa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 23
Onani Mateyu 23:25 nkhani