31 Koma pamene Mwana wa munthu adzadza mu ulemerero wace, ndi angelo onse pamodzi naye, pomwepo Iye adzakhala pa cimpando ca kuwala kwace:
Werengani mutu wathunthu Mateyu 25
Onani Mateyu 25:31 nkhani