Mateyu 25:32 BL92

32 ndipo adzasonkhanidwa pamaso pace anthu a mitundu yonse; ndipo Iye adzalekanitsa iwo wina ndi mnzace, monga mbusa alekanitsa nkhosa ndi mbuzi;

Werengani mutu wathunthu Mateyu 25

Onani Mateyu 25:32 nkhani