43 ndinali mlendo, ndipo simunandilandira Ine; wamarisece ndipo simunandibveka Ine; wodwala, ndi m'nyumba yandende, ndipo simunadza kundiona Ine.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 25
Onani Mateyu 25:43 nkhani