Mateyu 26:1 BL92

1 Ndipo panali pamene Yesu anatha mau onse amenewa, anati kwa ophunzira ace,

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:1 nkhani