46 Ndipo amenewa adzacoka kumka ku cilango ca nthawi zonse; koma olungama ku moyo wa nthawi zonse.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 25
Onani Mateyu 25:46 nkhani