45 Pomwepo Iye adzayankha iwo kuti, Indetu ndinena kwa inu, Cifukwa munalibe kucitira ici mmodzi wa awa ang'onong'ono, munalibe kundicitira ici Ine.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 25
Onani Mateyu 25:45 nkhani