Mateyu 26:21 BL92

21 ndipo m'mene analinkudya, Iye anati, Indetu ndinena kwa inu, mmodzi wa inu adzandipereka Ine.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:21 nkhani