23 Ndipo Iye anayankha nati, Iye amene asunsa pamodzi ndi Ine dzanja lace m'mbale, yemweyu adzandipereka Ine.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:23 nkhani