Mateyu 26:24 BL92

24 Mwana wa munthu acokatu, monga kunalembedwa za Iye; koma tsoka ali nalo munthu amene Mwana wa munthu aperekedwa ndi iye! kukadakhala bwino kwa munthuyo ngati sakadabadwa.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:24 nkhani