Mateyu 26:33 BL92

33 Koma Petro ananena kwa Iye, Ngakhale onse adzakhumudwa cifukwa ca Inu, ine sindidzakhumudwa nthawi zonse.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:33 nkhani