42 Anamukanso kaciwiri, napemphera, nati, Atate wanga, ngati ici sicingandipitirire, koma ndimwere ici, kufuna kwanu kucitidwe.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:42 nkhani