Mateyu 26:48 BL92

48 Koma wompereka Iye anawapatsa cizindikiro, nanena, Iye amene ndidzampsompsona ndiyeyo, mumgwire Iye.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:48 nkhani