Mateyu 26:50 BL92

50 Ndipo Yesu anati kwa iye, Mnzanga, wafikiranji: iwe? Pomwepo iwo anadza, namthira Yesu manja, namgwira Iye.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:50 nkhani