51 Ndipo onani, mmodzi wa iwo anali pamodzi ndi Yesu, anatansa dzanja lace, nasolola Iupanga lace, nakantha kapolo wa mkuru wa ansembe, nadula khutu lace.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:51 nkhani