56 Koma izi zonse zinacitidwa, kuti 1 zolembedwa za aneneri zikwaniridwe. Pomwepo ophunzira onse anamsiya Iye, nathawa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:56 nkhani