Mateyu 26:57 BL92

57 Ndipo iwo akugwira Yesu anaaka naye kwa Kayafa, mkuru wa ansembe, kumene adasonkhana alembi ndi akuru omwe.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:57 nkhani