58 Koma Petro anamtsata kutari, kufikira ku bwalo la mkuru wa ansembe, nalowamo, nakhala pansi ndi anyamata, kuti aone cimariziro.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:58 nkhani