7 anadza kwa Iye mkazi, anali nayo nsupa yaalabastero ndi mafuta onunkhira bwino a mtengo wapatari, nawatsanulira pamutu pace, m'mene Iye analikukhala pacakudya.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:7 nkhani