23 Onse anati, Apacikidwe pamtanda. Ndipo iye anati, Cifukwa ninji? anacita coipa cotani? Koma iwo anapfuulitsa kopambana, Apacikidwe pamtanda.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 27
Onani Mateyu 27:23 nkhani