Mateyu 27:3 BL92

3 Pamenepo Yudase yemwe anampereka Iye, poona kuti Iye anatsutsidwa kuti afe, analapa, nabweza ndalama zija zasiliva makumi atatu kwa ansembe akuru ndi akuru,

Werengani mutu wathunthu Mateyu 27

Onani Mateyu 27:3 nkhani