4 nanena, Ndinacita koipa ine, pakupereka mwazi wosalakwa. Koma iwo anati, Tiri naco ciani ife? udzionere wekha.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 27
Onani Mateyu 27:4 nkhani