56 mwa iwo 13 amene munali Mariya wa Magadala, ndi Mariya amace wa Yakobo, ndi wa Yose, ndi amace wa ana a Zebedayo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 27
Onani Mateyu 27:56 nkhani