Mateyu 27:57 BL92

57 Ndipo pamene panali madzulo, anadza munthu wacuma wa ku Arimateya, dzina lace Yosefe, amene analinso wophunzira wa Yesu;

Werengani mutu wathunthu Mateyu 27

Onani Mateyu 27:57 nkhani