Mateyu 27:6 BL92

6 Ndipo ansembe akuru anatenga ndalamazo, nati, Sikuloledwa kuziika m'cosonkhera ndalama za Mulungu, cifukwa ndizo mtengo wa mwazi.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 27

Onani Mateyu 27:6 nkhani