Mateyu 28:1 BL92

1 Ndipo popita dzuwa la Sabata, mbanda kuca, tsiku lakuyamba la sabata, anadza Mariya wa Magadala, ndi Mariya winayo, kudzaona manda.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 28

Onani Mateyu 28:1 nkhani