Mateyu 28:2 BL92

2 Ndipo onani, panali cibvomezi cacikuru; pakuti mngelo wa Ambuye anatsika Kumwamba, nafika kukunkhuniza mwalawo, nakhala pamwamba pace.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 28

Onani Mateyu 28:2 nkhani