5 Koma mngelo anayankha, nati kwa akaziwo, Musaope inu; pakuti ndidziwa inu mulikufuna Yesu, amene anapacikidwa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 28
Onani Mateyu 28:5 nkhani