6 Iye mulibe muno iai; pakuti anauka, monga ananena. Idzani muno mudzaone malo m'mene anagonamo Ambuye.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 28
Onani Mateyu 28:6 nkhani