Mateyu 28:7 BL92

7 Ndipo pitani msanga, muuze ophunzira ace, kuti, Wauka kwa akufa; ndipo onani, akutsogolerani ku Galileya; mudzamuona Iye komweko; onani, ndakuuzani inu.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 28

Onani Mateyu 28:7 nkhani