Mateyu 6:23 BL92

23 Koma ngati diso lako liri loipa, thupi lako lonse lidzakhala lodetsedwa. Cifukwa cace ngati kuwala kumene kuli mwa inu kuli mdima, mdimawo ndi waukuru ndithu!

Werengani mutu wathunthu Mateyu 6

Onani Mateyu 6:23 nkhani