28 Ndipo muderanji nkhawa ndi cobvala? Tapenyetsani maluwa a kuthengo, makulidwe ao; sagwiritsa nchito, kapena sapota:
Werengani mutu wathunthu Mateyu 6
Onani Mateyu 6:28 nkhani