29 koma ndinena kwa inu, kuti angakhale Solomo mu ulemerero wace wonse sanabvala monga limodzi la amenewa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 6
Onani Mateyu 6:29 nkhani