Mateyu 6:30 BL92

30 Koma ngati Mulungu abveka cotero maudzu a kuthengo, akhala lero, ndi mawa oponyedwa pamoto, nanga si inu kopambana ndithu, inu akukhulupirira pang'ono?

Werengani mutu wathunthu Mateyu 6

Onani Mateyu 6:30 nkhani