Mateyu 7:13 BL92

13 Lowani pa cipata copapatiza; cifukwa cipata ciri cacikuru, ndi njira yakumuka nayo kukuonongeka iri yotakata; ndipo ali ambiri amene alowa pa ico.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 7

Onani Mateyu 7:13 nkhani