14 Pakuti cipata ciri copapatiza, ndi icepetsa njirayo yakumuka nayo kumoyo, ndimo akucipeza cimeneco ali owerengeka.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 7
Onani Mateyu 7:14 nkhani