Mateyu 8:12 BL92

12 koma anawo a Ufumu adzatayidwa ku mdima wakunja; komweko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 8

Onani Mateyu 8:12 nkhani